Yohane 18:27 - Buku Lopatulika27 Pamenepo Petro anakananso; ndipo pomwepo analira tambala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Pamenepo Petro anakananso; ndipo pomwepo analira tambala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Petro adakananso, nthaŵi yomweyo tambala adalira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Petro anakananso, ndipo pa nthawi yomweyo tambala analira. Onani mutuwo |