Yohane 18:26 - Buku Lopatulika26 Mmodzi wa akapolo a mkulu wa ansembe ndiye mbale wake uja amene Petro anamdula khutu, ananena, Ine sindinakuone iwe kodi m'munda pamodzi ndi Iye? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Mmodzi wa akapolo a mkulu wa ansembe ndiye mbale wake uja amene Petro anamdula khutu, ananena, Ine sindinakuona iwe kodi m'munda pamodzi ndi Iye? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Wantchito wina wa mkulu wa ansembe onse, mbale wa munthu uja amene Petro adaamusenga khutu, adamufunsa kuti, “Kodi sindidakuwone m'munda muja uli naye?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Mmodzi wa antchito a mkulu wa ansembe, mʼbale wa munthu amene anadulidwa khutu ndi Petro anamutsutsa iye kuti, “Kodi sindinakuone iwe pamodzi ndi Iye mʼmunda muja?” Onani mutuwo |