Yohane 18:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo mkulu wa ansembe anafunsa Yesu za ophunzira ake, ndi chiphunzitso chake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo mkulu wa ansembe anafunsa Yesu za ophunzira ake, ndi chiphunzitso chake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Tsono mkulu wa ansembe onse adafunsa Yesu za ophunzira ake, ndiponso za zimene Iye ankaphunzitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Pa nthawi imeneyi, mkulu wa ansembe anamufunsa Yesu za ophunzira ake ndi chiphunzitso chake. Onani mutuwo |