Yohane 16:31 - Buku Lopatulika31 Yesu anayankha iwo, Kodi mukhulupirira tsopano? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Yesu anayankha iwo, Kodi mukhulupirira tsopano? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Yesu adaŵayankha kuti, “Kani mwakhulupiriratu tsopano? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Yesu anawafunsa kuti, “Kodi tsopano mwakhulupirira?” Onani mutuwo |