Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yohane 16:29 - Buku Lopatulika

29 Ophunzira ake ananena, Onani, tsopano mulankhula zomveka, ndipo mulibe kunena chiphiphiritso.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Ophunzira ake ananena, Onani, tsopano mulankhula zomveka, ndipo mulibe kunena chiphiphiritso.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Ophunzira ake adati, “Apo ndipo. Tsopano mukulankhula momveka, osatinso mophiphiritsa ai.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 Kenaka ophunzira ake anati, “Tsopano mukuyankhula momveka bwino ndi mopanda mafanizo.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 16:29
4 Mawu Ofanana  

Zonsezi Yesu anaziphiphiritsira m'mafanizo kwa makamu a anthu; ndipo kopanda fanizo sanalankhule kanthu kwa iwo;


Ndipo mauwo ananena poyera. Ndipo Petro anamtenga Iye, nayamba kumdzudzula.


Fanizo ili Yesu ananena kwa iwo; koma sanazindikire zimene Yesu analikulankhula nao.


Zinthu izi ndalankhula ndi inu m'mafanizo; ikudza nthawi imene sindidzalankhula ndi inu m'mafanizo, koma ndidzakulalikirani inu m'mafanizo, koma ndidzakulalikirani inu momveka za Atate.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa