Yohane 16:15 - Buku Lopatulika15 Zinthu zilizonse Atate ali nazo ndi zanga; chifukwa chake ndinati, kuti atenga za mwa Ine, nadzalalikira kwa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Zinthu zilizonse Atate ali nazo ndi zanga; chifukwa chake ndinati, kuti atenga za mwa Ine, nadzalalikira kwa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Zonse za Atate nzanga. Nchifukwa chake ndanena kuti adzatenga zochokera kwa Ine, nadzakudziŵitsani inu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Zonse za Atate ndi zanga. Ichi nʼchifukwa chake Ine ndanena kuti Mzimu Woyera adzatenga kwa Ine zanga kuti muzidziwe.” Onani mutuwo |