Yohane 15:25 - Buku Lopatulika25 Koma chitero, kuti mau olembedwa m'chilamulo chao akwaniridwe, kuti, Anandida Ine kopanda chifukwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Koma chitero, kuti mau olembedwa m'chilamulo chao akwaniridwe, kuti, Anandida Ine kopanda chifukwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Koma zatere kuti zipherezere zimene zidalembedwa m'buku lao la Malamulo kuti, ‘Adadana nane popanda chifukwa.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Koma zatere kuti zikwaniritse zimene zinalembedwa mʼmalamulo awo: ‘Iwo anandida Ine popanda chifukwa.’ Onani mutuwo |