Yohane 15:17 - Buku Lopatulika17 Zinthu izi ndilamula inu, kuti mukondane wina ndi mnzake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Zinthu izi ndilamula inu, kuti mukondane wina ndi mnzake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Choncho lamulo langa ndi lakuti muzikondana.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Lamulo langa ndi ili: ‘Muzikondana.’ Onani mutuwo |