Yohane 14:29 - Buku Lopatulika29 Ndipo tsopano ndakuuzani chisanachitike, kuti pamene chitachitika mukakhulupirire. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndipo tsopano ndakuuzani chisanachitike, kuti pamene chitachitika mukakhulupirire. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Ndakuuziranitu zimenezi tsopano zisanachitike, kuti zikadzachitika, mudzakhulupirire. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Ine ndakuwuzani tsopano zisanachitike, kuti zikadzachitika mudzakhulupirire. Onani mutuwo |