Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yohane 14:14 - Buku Lopatulika

14 Ngati mudzapempha kanthu m'dzina langa, ndidzachita.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Ngati mudzapempha kanthu m'dzina langa, ndidzachita.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Ngati mudzandipempha kanthu potchula dzina langa ndidzakachitadi.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Ngati mudzapempha kanthu kalikonse mʼdzina langa, Ine ndidzachita.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 14:14
6 Mawu Ofanana  

Ndipo chimene chilichonse mukafunse m'dzina langa, ndidzachichita, kuti Atate akalemekezedwe mwa Mwana.


Ndipo Ine ndidzapempha Atate, ndipo adzakupatsani inu Nkhoswe ina, kuti akhale ndi inu kunthawi yonse,


Inu simunandisankhe Ine, koma Ine ndinakusankhani inu, ndipo ndinakuikani, kuti mukamuke inu ndi kubala chipatso, ndi kuti chipatso chanu chikhale; kuti chimene chilichonse mukapempha Atate m'dzina langa akakupatseni inu.


Ndipo tsiku limenelo simudzandifunsa kanthu. Indetu, indetu, ndinena kwa inu, Ngati mudzapempha Atate kanthu, adzakupatsani inu m'dzina langa.


Kufikira tsopano simunapemphe kanthu m'dzina langa; pemphani, ndipo mudzalandira, kuti chimwemwe chanu chikwaniridwe.


Ndiyamika Mulungu wanga nthawi yonse kaamba ka inu, chifukwa cha chisomo cha Mulungu chinapatsidwa kwa inu mwa Khristu Yesu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa