Yohane 13:38 - Buku Lopatulika38 Yesu anayankha, Moyo wako kodi udzautaya chifukwa cha Ine? Indetu, indetu, ndinena kwa iwe, Asanalire tambala udzandikana Ine katatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Yesu anayankha, Moyo wako kodi udzautaya chifukwa cha Ine? Indetu, indetu, ndinena kwa iwe, Asanalire tambala udzandikana Ine katatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Apo Yesu adati, “Iweyo kutaya moyo wako chifukwa cha Ine! Ndithu ndikunenetsa kuti tambala asanalire, ukhala utandikana katatu kuti Ine sundidziŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Kenaka Yesu anayankha kuti, “Kodi iwe udzalolera kutaya moyo chifukwa cha Ine? Zoonadi, Ine ndikukuwuza kuti tambala asanalire, iwe udzandikana katatu!” Onani mutuwo |