Yohane 13:37 - Buku Lopatulika37 Petro ananena ndi Iye, Ambuye, sindingathe kukutsatani Inu tsopano chifukwa ninji? Ndidzataya moyo wanga chifukwa cha Inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Petro ananena ndi Iye, Ambuye, sindingathe kukutsatani Inu tsopano chifukwa ninji? Ndidzataya moyo wanga chifukwa cha Inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 Petro adamufunsa kuti, “Ambuye, chifukwa chiyani sindingathe kukutsatirani tsopano? Inetu nditha kutaya ngakhale moyo wanga chifukwa cha Inu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Petro anafunsa kuti, “Ambuye, nʼchifukwa chiyani ine sindingakutsatireni tsopano? Ine ndidzapereka moyo wanga chifukwa cha Inu.” Onani mutuwo |