Yohane 13:33 - Buku Lopatulika33 Tiana, katsala kanthawi ndikhala ndi inu. Mudzandifunafuna Ine; ndipo monga ndinanena kwa Ayuda, kuti kumene ndinkako Ine, inu simungathe kudza, momwemo ndinena kwa inu tsopano. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Tiana, katsala kanthawi ndikhala ndi inu. Mudzandifunafuna Ine; ndipo monga ndinanena kwa Ayuda, kuti kumene ndinkako Ine, inu simungathe kudza, momwemo ndinena kwa inu tsopano. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Ana anga, ndili nanube kanthaŵi pang'ono. Mudzandifunafuna, koma ndikukuuzani tsopano, monga ndidauziranso akulu a Ayuda kuti, ‘Kumene ndikupita Ine, inu simungathe kufikako.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 “Ana anga, Ine ndikhala nanu kwa nthawi yochepa chabe. Inu mudzandifunafuna Ine, ndipo monga momwe ndinawawuzira Ayuda, choncho Ine ndikukuwuzani tsopano kuti, kumene Ine ndikupita, inu simungabwereko. Onani mutuwo |