Yohane 13:28 - Buku Lopatulika28 Koma palibe mmodzi wa iwo akuseamako anadziwa chimene anafuna, poti atere naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Koma palibe mmodzi wa iwo akuseamako anadziwa chimene anafuna, poti atere naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Koma mwa amene ankadyawo panalibe ndi mmodzi yemwe amene adaamvetsa zimene adaamuuzazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Koma panalibe ndi mmodzi yemwe pa chakudyapo amene anamvetsa chifukwa chimene Yesu ananenera izi kwa iye. Onani mutuwo |