Yohane 12:37 - Buku Lopatulika37 Koma angakhale adachita zizindikiro zambiri zotere pamaso pao iwo sanakhulupirire Iye; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Koma angakhale adachita zizindikiro zambiri zotere pamaso pao iwo sanakhulupirira Iye; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 Ngakhale Yesu adaachita zozizwitsa zambiri chotere pamaso pao, komabe iwo sadamkhulupirire. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Ngakhale Yesu anachita zizindikiro zodabwitsa zonsezi pamaso pawo, sanamukhulupirirebe. Onani mutuwo |