Yohane 12:36 - Buku Lopatulika36 Pokhala muli nako kuunika, khulupirirani kuunikako, kuti mukakhale ana a kuunikako. Izi Yesu analankhula, nachoka nawabisalira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Pokhala muli nako kuunika, khulupirirani kuunikako, kuti mukakhale ana a kuunikako. Izi Yesu analankhula, nachoka nawabisalira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Nthaŵi ino pamene kuŵala kuli pakati panu, mukhulupirire kuŵalako, kuti mukhale anthu oyenda m'kuŵala.” Yesu atanena zimenezi, adachokapo nakabisala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Khulupirirani kuwunika, pamene mukanali ndi kuwunika, kuti mukhale ana a kuwunika.” Yesu atamaliza kuyankhula izi, Iye anachoka nabisala kuti asamuone. Onani mutuwo |