Yohane 12:33 - Buku Lopatulika33 Koma ananena ichi ndi kuzindikiritsa imfa yanji akuti adzafa nayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Koma ananena ichi ndi kuzindikiritsa imfa yanji akuti adzafa nayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 (Adaanena mau ameneŵa kuti aŵadziŵitse za m'mene analikudzafera.) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Iye ananena izi kuti aonetse mmene adzafere. Onani mutuwo |