Yohane 11:50 - Buku Lopatulika50 kapena simuganiza kuti nkokoma kwa inu kuti munthu mmodzi afere anthu, ndi kuti mtundu wonse usaonongeke. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201450 kapena simuganiza kuti nkokoma kwa inu kuti munthu mmodzi afere anthu, ndi kuti mtundu wonse usaonongeke. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa50 Monga inu simukuwona kuti nkwabwino koposa kwa inu kuti munthu mmodzi afere anthu onse, m'malo moti mtundu wathu wonse uwonongeke?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero50 Inu simukuzindikira kuti kuli bwino kwa inu kuti munthu mmodzi afe mʼmalo mwa anthu kusiyana ndi kuti mtundu wonse uwonongeke.” Onani mutuwo |