Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yohane 11:46 - Buku Lopatulika

46 Koma ena a mwa iwo anamuka kwa Afarisi, nawauza zimene Yesu adazichita.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

46 Koma ena a mwa iwo anamuka kwa Afarisi, nawauza zimene Yesu adazichita.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

46 Koma ena adapita kwa Afarisi, nakaŵasimbira zimene Yesu adaachita.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

46 Koma ena a iwo anapita kwa Afarisi ndi kukawawuza zimene Yesu anachita.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 11:46
8 Mawu Ofanana  

Koma ansembe aakulu ndi Afarisi adalamula kuti, munthu wina akadziwa pokhala Iye, aulule, kuti akamgwire Iye.


Koma angakhale adachita zizindikiro zambiri zotere pamaso pao iwo sanakhulupirire Iye;


Afarisi anamva khamu la anthu ling'ung'udza zimenezi za Iye; ndipo ansembe aakulu ndi Afarisi anatuma anyamata kuti akamgwire Iye.


Pamenepo anyamatawo anadza kwa ansembe aakulu ndi Afarisi; ndipo iwowa anati kwa iwo, Simunamtenge Iye bwanji?


Anapita naye amene anali wosaona kale kwa Afarisi.


Ndipo anadza wina nawafotokozera, kuti, Taonani, amuna aja mudawaika m'ndende ali mu Kachisi, alikuimirira ndi kuphunzitsa anthu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa