Yohane 11:45 - Buku Lopatulika45 Chifukwa chake ambiri a mwa Ayuda amene anadza kwa Maria, m'mene anaona chimene anachita, anakhulupirira Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Chifukwa chake ambiri a mwa Ayuda amene anadza kwa Maria, m'mene anaona chimene anachita, anakhulupirira Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Ambiri mwa anthu amene adaabwera kwa Maria, adaona zimene Yesu adaachita, ndipo adamkhulupirira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Choncho Ayuda ambiri amene anabwera kudzamuchereza Mariya ndi kuona zimene Yesu anachita anamukhulupirira Iye. Onani mutuwo |