Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 8:5 - Buku Lopatulika

5 koma ukafunitsitsa Mulungu, ndi kupembedza Wamphamvuyonse;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 koma ukafunitsitsa Mulungu, ndi kupembedza Wamphamvuyonse;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Ngati iwe uchita zimene Mulungu afuna, ngati upemba kwa Mphambe,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Koma utayangʼana kwa Mulungu, ndi kudandaulira Wamphamvuzonse,

Onani mutuwo Koperani




Yobu 8:5
10 Mawu Ofanana  

Ukakonzeratu mtima wako, ndi kumtambasulira Iye manja ako;


Taona, wodala munthu amene Mulungu amdzudzula; chifukwa chake usapeputsa kulanga kwa Wamphamvuyonse.


Koma ine ndikadafuna Mulungu, ndikadaikira mlandu wanga Mulungu;


Ameneyo, chinkana ndikadakhala wolungama, sindikadamyankha; ndikadangompembedza wondiweruza ine.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa