Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 8:4 - Buku Lopatulika

4 Chinkana ana ako anamchimwira Iye, ndipo anawapereka mwa kulakwa kwao;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Chinkana ana ako anamchimwira Iye, ndipo anawapereka mwa kulakwa kwao;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Kapena ana ako adamchimwira, nkuwona Mulungu adaŵalanga chifukwa cha zochimwa zaozo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Pamene ana ako anamuchimwira Mulungu, Iye anawapereka kuti alangidwe chifukwa cha tchimo lawo.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 8:4
8 Mawu Ofanana  

Ndipo anthu a ku Sodomu anali oipa ndi ochimwa kwambiri pamaso pa Yehova.


Ndipo kunatero, atatha masiku a madyererowa Yobu anatumiza mau, nawapatula, nauka mamawa, nafukiza nsembe zopsereza, monga mwa kuwerenga kwa iwo onse; pakuti Yobu anati, Kapena anachimwa ana anga, nachitira Mulungu mwano m'mtima mwao, Anatero Yobu masiku onse.


Ana ake akhala otekeseka, napsinjika kuchipata, wopanda wina wakuwapulumutsa.


Potero ndinawaperekera kuuma mtima kwao, ayende monga mwa uphungu waowao.


Taonani, miyoyo yonse ndi yanga, monga moyo wa atate momwemonso moyo wa mwana, ndiyo yanga; moyo wochimwawo ndiwo udzafa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa