Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 7:8 - Buku Lopatulika

8 Diso la amene andiona silidzandionanso, maso ako adzandipenyetsetsa, koma ine palibe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Diso la amene andiona silidzandionanso, maso ako adzandipenyetsetsa, koma ine palibe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Amene akundiwona tsopano, sadzandiwonanso. Nthaŵi yomwe iye adzandifunafuna, ine ndidzakhala nditapita.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Amene akundiona tsopano akundiona; mudzandifunafuna koma sindidzapezekanso.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 7:8
14 Mawu Ofanana  

Koma tsopano wafa, ndidzasaliranjinso kudya? Kodi ndikhoza kumbweza? Ine ndidzamuka kuli iye, koma iye sadzabweranso kwa ine.


Mulonganso mapazi anga m'zigologolo, ndi kupenyerera mayendedwe anga onse; mudzilembera malire mopanika mapazi anga.


Koma munthu akufa atachita liondeonde inde, munthu apereka mzimu wake, ndipo ali kuti?


Ndipo kodi mumtsegulira maso anu wotereyo, ndi kunditenga kunena nane mlandu Inu?


Adzauluka ngati loto, osapezekanso; nadzaingidwa ngati masomphenya a usiku.


Diso lidamuonalo silidzamuonanso; ndi malo ake sadzampenyanso.


Agona pansi ali wachuma, koma saikidwa; potsegula maso ake, wafa chikomo.


Pakuti ndikadagona pansi pomwepo ndi kukhala chete; ndikanagona tulo; pamenepo ndikadaona popumula;


Mulekeranji kukhululukira kulakwa kwanga ndi kundichotsera mphulupulu yanga? Popeza tsopano ndidzagona kufumbi; mudzandifunafuna, koma ine palibe.


Akamuononga kumchotsa pamalo pake, padzamkana, ndi kuti, Sindinakuone.


Pakuti mphepo ikapitapo pakhala palibe: Ndi malo ake salidziwanso.


Koma anapita ndipo taona, kwati zii; ndipo ndinampwaira osampeza.


Pamene mulanga munthu ndi zomdzudzula chifukwa cha mphulupulu, mukanganula kukongola kwake monga mumachita ndi njenjete. Indedi, munthu aliyense ali chabe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa