Yobu 6:3 - Buku Lopatulika3 Pakuti zikadalemera tsopano koposa mchenga wa kunyanja; chifukwa chake mau anga ndasonthokera kunena. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pakuti zikadalemera tsopano koposa mchenga wa kunyanja; chifukwa chake mau anga ndasonthokera kunena. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 bwenzi atalemera kupambana mchenga wonse wam'nyanja. Nchifukwa chake kulankhula kwanga kuli kokadzulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ndithu, zikanalemera kupambana mchenga wa ku nyanja; nʼchifukwa chake mawu anga akhala okhadzula. Onani mutuwo |