Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 6:2 - Buku Lopatulika

2 Mwenzi atayesa bwino chisoni changa, ndi kuika matsoka anga pamodzi pamuyeso!

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Mwenzi atayesa bwino chisoni changa, ndi kuika matsoka anga pamodzi pamuyeso!

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 “Achikhala mavuto anga adaayesedwa, achikhala masoka anga adaaŵaika pa sikelo,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 “Achikhala mavuto anga anayezedwa, ndipo zipsinjo zanga zonse zikanayikidwa pa sikelo!

Onani mutuwo Koperani




Yobu 6:2
5 Mawu Ofanana  

Lero lomwe kudandaula kwanga kumawawa; kulanga kwanga kuposa kubuula kwanga m'kulemera kwake.


andiyese ndi muyeso wolingana, kuti Mulungu adziwe ungwiro wanga.


Koma tsopano chakufikira iwe, ndipo ukomoka; chikukhudza, ndipo uvutika.


Koma Yobu anayankha, nati,


Mtima udziwa kuwawa kwakekwake; mlendo sadudukira ndi chimwemwe chake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa