Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 5:3 - Buku Lopatulika

3 Ndinapenya wopusa woyala mizu; koma pomwepo ndinatemberera pokhala pake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndinapenya wopusa woyala mizu; koma pomwepo ndinatemberera pokhala pake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Ine ndidaona chitsiru chitamera mizu, koma mwadzidzidzi nyumba yake ndidaitemberera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Ine ndinaona chitsiru chitamera mizu, koma mwadzidzidzi nyumba yake inatembereredwa.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 5:3
12 Mawu Ofanana  

Atengedwa ngati choyandama pamadzi; gawo lao litembereredwa padziko; sadzalunjikanso njira ya minda yampesa.


Pakuti chiyembekezo cha wonyoza Mulungu nchiyani pomlikhatu Mulungu, pomchotsera moyo wake?


ndithu sindinalole m'kamwa mwanga muchimwe, kupempha motemberera moyo wake.


Pakuti iwo amene awadalitsa adzalandira dziko lapansi; koma iwo amene awatemberera adzadulidwa.


Pokhala pao pakhale bwinja; m'mahema mwao musakhale munthu.


chakuti pophuka oipa ngati msipu, ndi popindula ochita zopanda pake; chitero kuti adzaonongeke kosatha.


Pakuti kwalembedwa m'buku la Masalimo, Pogonera pake pakhale bwinja, ndipo pasakhale munthu wogonapo; ndipo uyang'aniro wake autenge wina.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa