Yobu 5:1 - Buku Lopatulika1 Itana tsono; pali wina wakukuyankha kodi? Ndipo udzatembenukira kwa yani wa oyera mtimawo? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Itana tsono; pali wina wakukuyankha kodi? Ndipo udzatembenukira kwa yani wa oyera mtimawo? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 “Iwe Yobe, itana tsono. Kodi alipo wina aliyense adzakuyankhe? Kodi ndi kwa mngelo uti ungapeze thandizo? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 “Itana ngati ungathe, koma ndani adzakuyankhe? Kodi ndi kwa mngelo uti ungapezeko thandizo? Onani mutuwo |