Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 41:3 - Buku Lopatulika

3 Kodi idzachulukitsa mau akukupembedza? Kapena idzanena nawe mau ofatsa?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Kodi idzachulukitsa mau akukupembedza? Kapena idzanena nawe mau ofatsa?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Kodi chidzakupempha kuti uchimasule? Kodi chidzakupemba kuti uchichitire chifundo?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Kodi ngʼonayo idzakupempha kuti uyichitire chifundo? Kodi idzakuyankhula ndi mawu ofatsa?

Onani mutuwo Koperani




Yobu 41:3
10 Mawu Ofanana  

Kodi ukhoza kumanga m'mphuno ndi mlulu? Kapena kuboola nsagwada wake ndi mbedza?


Kodi idzapangana ndi iwe, kuti uitenge ikhale kapolo wako wachikhalire?


Dziko lapansi nla Yehova ndi zodzala zake zomwe, dziko lokhalamo anthu ndi iwo okhala m'mwemo.


Pakamwa pake mposalala ngati mafuta amkaka, koma mumtima mwake munali nkhondo, mau ake ngofewa ngati mafuta oyenga, koma anali malupanga osololasolola.


Ndipo tsopano, ngati mudzamvera mau anga ndithu, ndi kusunga chipangano changa, ndidzakuyesani chuma changa cha padera koposa mitundu yonse ya anthu; pakuti dziko lonse lapansi ndi langa;


Mayankhidwe ofatsa abweza mkwiyo; koma mau owawitsa aputa msunamo.


Wosauka amadandaulira; koma wolemera ayankha mwaukali.


Chipiriro chipembedza mkulu; lilime lofatsa lithyola fupa.


amene amati kwa alauli, Mtima wanu usapenye; ndi kwa aneneri, Musanenere kwa ife zinthu zoona, munene kwa ife zinthu zamyadi, munenere zonyenga;


Siliva ndi wanga, golide ndi wanga, ati Yehova wa makamu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa