Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 41:2 - Buku Lopatulika

2 Kodi ukhoza kumanga m'mphuno ndi mlulu? Kapena kuboola nsagwada wake ndi mbedza?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Kodi ukhoza kumanga m'mphuno ndi mlulu? Kapena kuboola nsagwada wake ndi mbedza?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Kodi ungathe kuchimanga chingwe m'mphuno mwake, kapena kuchiboola nsagwada ndi mbedza?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Kodi ungathe kumanga chingwe mʼmphuno mwake, kapena kubowola nsagwada zake ndi mbedza?

Onani mutuwo Koperani




Yobu 41:2
7 Mawu Ofanana  

Chifukwa cha kundizazira kwako, ndi popeza kudzikuza kwako kwandifikira m'makutu mwanga, ndidzakukowa ndi ngowe yanga m'mphuno mwako, ndi cham'kamwa changa m'milomo mwako; ndipo ndidzakubwezera panjira unadzerayi.


Kodi idzachulukitsa mau akukupembedza? Kapena idzanena nawe mau ofatsa?


Ndiye wa mtima wanzeru, ndi wa mphamvu yaikulu; ndaniyo anadziumitsa mtima pa Iye, nakhala nao mtendere?


Kulibe nzeru ngakhale luntha ngakhale uphungu wotsutsana ndi Yehova.


Tsiku limenelo Yehova ndi lupanga lake lolimba ndi lalikulu ndi lamphamvu adzalanga Leviyatani njoka yothamanga, ndi Leviyatani njoka yopindikapindika; nadzapha ching'ona chimene chili m'nyanja.


Chifukwa cha kundikwiyira Ine kwako, ndi popeza kudzikweza kwako kwafika m'makutu mwanga. Ine ndidzaika mbedza yanga m'mphuno mwako, ndi chapakamwa changa m'milomo yako, ndipo ndidzakubweza iwe m'njira yomwe unadzerayo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa