Yobu 41:1 - Buku Lopatulika1 Kodi ukhoza kukoka Leviyatani ndi mbedza? Kapena kukanikiza kalandira wake ndi chingwe? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Kodi ukhoza kukoka Leviyatani ndi mbedza? Kapena kukanikiza kalandira wake ndi chingwe? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Kodi ungathe kuchikoka ndi mbedza ya nsomba chilombo chija cha Leviyatani, kapena kukanikiza lilime lake pansi ndi chingwe? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 “Kodi ungathe kukoka ngʼona ndi mbedza ya nsomba kapena kukanikiza lilime lake pansi ndi chingwe? Onani mutuwo |