Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 4:7 - Buku Lopatulika

7 Takumbukira tsopano, watayika ndani wosapalamula konse? Kapena oongoka mtima alikhidwa kuti?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Takumbukira tsopano, watayika ndani wosapalamula konse? Kapena oongoka mtima alikhidwa kuti?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 “Ganiza bwino tsopano: Kodi alipo munthu wosachimwa amene adaonongekapo nkale lonse? Nanga nkuti kumene udaona anthu olungama ataphedwa?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 “Ganiza bwino tsopano: Kodi munthu wosalakwa anawonongekapo nʼkale lonse? Nʼkuti kumene munthu wolungama mtima anaphedwa?

Onani mutuwo Koperani




Yobu 4:7
9 Mawu Ofanana  

Sasunga woipa akhale ndi moyo, koma awaninkha ozunzika zowayenera iwo.


Sawachotsera wolungama maso ake, koma pamodzi ndi mafumu pa mpando wao awakhazika chikhazikire, ndipo akwezeka.


Taona, Mulungu sakana munthu wangwiro; kapena kugwiriziza ochita zoipa.


Ndinali mwana ndipo ndakalamba; ndipo sindinapenye wolungama atasiyidwa, kapena mbumba zake zilinkupempha chakudya.


Ndaona zonsezi masiku anga achabe; pali wolungama angofa m'chilungamo chake, ndipo pali woipa angokhalabe ndi moyo m'kuipa kwake.


Koma pamene akunjawo anaona chilombocho chili lende padzanja lake, ananena wina ndi mnzake, Zoona munthuyu ndiye wambanda. Angakhale anapulumuka m'nyanja, chilungamo sichimlola akhale ndi moyo.


Ambuye adziwa kupulumutsa opembedza poyesedwa iwo, ndi kusunga osalungama kufikira tsiku loweruza akalangidwe;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa