Yobu 4:2 - Buku Lopatulika2 Munthu akayesa kunena nawe mau, kodi udzamva nao chisoni? Koma akhoza ndani kudziletsa kunena? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Munthu akayesa kunena nawe mau, kodi udzamva nao chisoni? Koma akhoza ndani kudziletsa kunena? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Iwe Yobe, kodi wina atakuyankha, ndiye kuti wakulakwira? Ah, koma ine ndekha sindingathe kukhala chete. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Ngati wina atakuyankha, kodi ungakhumudwe? Koma ndani angakhale chete wosayankhula? Onani mutuwo |