Yobu 4:10 - Buku Lopatulika10 Kubangula kwa mkango, ndi kulira kwa mkango waukali kwaletsedwa, ndi mano a misona ya mkango athyoledwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Kubangula kwa mkango, ndi kulira kwa mkango waukali kwaletsedwa, ndi mano a misona ya mkango athyoledwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Anthu oipa amakhuluma ngati mkango, koma Mulungu amaŵathyola mano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mikango imabangula ndi kulira, komabe mano a mikango yamphamvu amathyoledwa. Onani mutuwo |