Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 39:3 - Buku Lopatulika

3 Zithuntha, ziswa, zitaya zowawa zao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Zithuntha, ziswa, zitaya zowawa zao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Kodi ukuidziŵa nthaŵi imene zidzakhala tsonga nkuswa ana, kenaka nkutayiza?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Zimakhala tsonga ndi kuswa ana awo; pamenepo ululu wobereka nʼkutha.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 39:3
2 Mawu Ofanana  

Ukhoza kodi kuwerenga miyezi yakuzipitira, kapena udziwa nyengo yoti ziswane?


Ana ao akhala ojincha, akulira kuthengo, achoka osabwerera kwa amao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa