Yobu 39:2 - Buku Lopatulika2 Ukhoza kodi kuwerenga miyezi yakuzipitira, kapena udziwa nyengo yoti ziswane? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ukhoza kodi kuwerenga miyezi yakuzipitira, kapena udziwa nyengo yoti ziswane? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Kodi ungathe kuŵerenga miyezi imene zimakhala ndi bele? Kodi nthaŵi imene nyamazi zimaswa iwe umaidziŵa? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Kodi umawerenga miyezi imene zimakhala ndi bere? Kodi nthawi imene zimaswana iwe umayidziwa? Onani mutuwo |