Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 38:3 - Buku Lopatulika

3 Udzimangire m'chuuno tsono ngati mwamuna; ndikufunsa, undidziwitse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Udzimangire m'chuuno tsono ngati mwamuna; ndikufunsa, undidziwitse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Onetsa chamuna, ndidzakufunsa, ndipo undiyankhe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Onetsa chamuna; ndikufunsa ndipo undiyankhe.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 38:3
13 Mawu Ofanana  

Ndipo dzanja la Yehova linakhala pa Eliya; namanga iye za m'chuuno mwake, nathamanga m'tsogolo mwa Ahabu ku chipata cha Yezireele.


Angakhale andipha koma ndidzamlindira; komanso ndidzaumirira mayendedwe anga pamaso pake.


Pamenepo muitane, ndipo ndidzayankha; kapena ndinene ndine, ndipo mundiyankhe ndinu.


Ngati pali munthu wakumphunzitsa Mulungu nzeru? Popeza Iye aweruza mlandu iwo okwezeka.


Kodi wodzudzulayo atsutsane ndi Wamphamvuyonse? Wochita makani ndi Mulungu ayankhe.


Dzimangire m'chuuno tsono ngati mwamuna; ndidzakufunsa, undidziwitse.


Tamveranitu, ndidzanena ine, ndidzakufunsani, mundidziwitse.


Ndipo muziidya chotero: okwinda m'chuuno, nsapato zanu pa mapazi anu ndodo yanu m'dzanja lanu, ndipo muziidya msanga; ndiye Paska wa Yehova.


Amanga m'chuuno mwake ndi mphamvu, nalimbitsa mikono yake.


Koma iwe ukwinde m'chuuno mwako, nuuke, nunene kwa iwo zonse zimene ndikuuza iwe; usaope nkhope zao ndingakuopetse iwe pamaso pao.


Mwa ichi, podzimanga m'chuuno, kunena za mtima wanu, mukhale odzisunga, nimuyembekeze konsekonse chisomo chilikutengedwa kudza nacho kwa inu m'vumbulutso la Yesu Khristu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa