Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 32:4 - Buku Lopatulika

4 Ndipo Elihu analindira kulankhula ndi Yobu, popeza akulu misinkhu ndi iwowa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo Elihu analindira kulankhula ndi Yobu, popeza akulu misinkhu ndi iwowa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Koma Elihu adadikira kuti alankhule ndi Yobe, chifukwa choti abwenziwo anali akuluakulu kupambana iyeyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Tsono Elihu anadikira kuti ayankhule ndi Yobu chifukwa choti abwenziwo anali akuluakulu kupambana iyeyo.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 32:4
6 Mawu Ofanana  

Adapsa mtima pa mabwenzi ake atatu omwe, pakuti anasowa pomyankha; koma anamtsutsa Yobu kuti ali woipa.


Koma pakuona Elihu kuti anthu atatuwa anasowa poyankha pakamwa pao anapsa mtima.


Wobwezera mau asanamvetse apusa, nadzichititsa manyazi.


mphindi yakung'amba ndi mphindi yakusoka; mphindi yakutonthola ndi mphindi yakulankhula;


Pali aimvi uziwagwadira, nuchitire ulemu munthu wokalamba; nuope Mulungu wako; Ine ndine Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa