Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 32:1 - Buku Lopatulika

1 Pamenepo amuna atatuwa analeka kumyankha Yobu; pakuti anali wolungama pamaso pake pa iye mwini.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Pamenepo amuna atatuwa analeka kumyankha Yobu; pakuti anali wolungama pamaso pake pa iye mwini.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Tsono anthu atatu aja adaleka osamulankhuzanso Yobe, chifukwa choti iyeyo adaadziwona kuti ndi wosachimwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Tsono anthu atatuwa analeka kumuyankha Yobu, chifukwa chakuti iyeyo ankadziona kuti ndi wolungama.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 32:1
14 Mawu Ofanana  

Ndidzati kwa Mulungu, Musanditsutse; mundidziwitse chifukwa cha kutsutsana nane.


chinkana mudziwa kuti sindili woipa, ndipo palibe wakupulumutsa m'dzanja lanu?


Angakhale andipha koma ndidzamlindira; komanso ndidzaumirira mayendedwe anga pamaso pake.


Taonani tsono, ndalongosola mlandu wanga; ndidziwa kuti adzandimasula ndili wolungama.


Pakuti pakamwa pako paphunzitsa mphulupulu zako, nusankha lilime la ochenjerera.


Zoipa zako sizichuluka kodi? Ndi mphulupulu zako sizikhala zosawerengeka kodi?


Apo woongoka mtima akadatsutsana naye; ndipo ndikadapulumuka chipulumukire kwa Woweruza wanga.


Zedi mwanena m'makutu mwanga, ndinamvanso mau a kunena kwanu, akuti,


Ndine woyera ine, wopanda kulakwa, ndine wosapalamula, ndilibe mphulupulu.


Chingakhale chiweruzo changa udzachithyola kodi? Udzanditsutsa kuti ndili woipa kodi, kuti ukhale wolungama ndiwe?


Bwererani, ndikupemphani, musandiipsire mlandu; inde, bwereraninso mlandu wanga ngwolungama.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa