Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 3:9 - Buku Lopatulika

9 Nyenyezi za chizirezire zide; uyembekezere kuunika, koma kuusowe; usaone kephenyuka kwa mbandakucha;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Nyenyezi za chizirezire zide; uyembekezere kuunika, koma kuusowe; usaone kephenyuka kwa mbandakucha;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Nyenyezi zake zambandakucha zisaŵale. Tsikulo liyembekeze kucha, koma pachabe. Lisaonenso kuŵala kwa mbandakucha.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Nyenyezi zake za mʼbandakucha zikhale mdima; tsikulo liyembekezere kucha pachabe ndipo lisaonenso kuwala koyamba kwa mʼbandakucha.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 3:9
7 Mawu Ofanana  

popeza sunatseke pa makomo ake mimba ya mai wanga. Kapena kundibisira mavuto pamaso panga.


Autemberere iwo akutemberera usana, Odziwa kuutsa Leviyatani.


Muja ndinayembekeza chokoma chinadza choipa, ndipo polindira kuunika unadza mdima.


Palibe wolimba mtima kuti adzaiputa. Ndipo ndaniyo adzaima pamaso pa Ine?


Pakuyetsemula ing'anipitsa kuunika, ndi maso ake akunga zikope za m'mawa.


Lemekezani Yehova Mulungu wanu, kusanade, mapazi anu asanaphunthwe pa mapiri achizirezire; nimusanayembekeze kuunika, Iye asanasandutse kuunikaku mthunzi wa imfa, ndi kukuyesa mdima wa bii.


Tinayang'anira mtendere, koma panalibe zabwino; ndi nthawi ya moyo, ndipo taona kuopsedwa!


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa