Yobu 3:6 - Buku Lopatulika6 Usiku uja, mdima weniweni uugwere; usakondwerere mwa masiku a m'chaka; usalowe m'chiwerengedwe cha miyezi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Usiku uja, mdima weniweni uugwere; usakondwerere mwa masiku a m'chaka; usalowe m'chiwerengedwe cha miyezi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Usiku umenewo ukhale wa mdima wandiweyani. Tsiku limenelo lisakhalenso pamodzi ndi masiku a pa chaka, lisaŵerengedwerenso kumodzi ndi masiku a pa miyezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Usiku umenewo ukutidwe ndi mdima wandiweyani; usawerengedwenso pamodzi ndi masiku a chaka, kapena kukhala pa mwezi wina uliwonse. Onani mutuwo |