Yobu 3:3 - Buku Lopatulika3 Litayike tsiku lobadwa ine, ndi usikuwo udati, Waima naye mwana wamwamuna. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Litayike tsiku lobadwa ine, ndi usikuwo udati, Waima naye mwana wamwamuna. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 “Tsiku limene ine ndidabadwa litembereredwe, nawonso usiku umene mai wanga adatenga pathupi pa ine utembereredwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 “Tsiku limene ine ndinabadwa litembereredwe ndi usiku umene ananena kuti, ‘Mwana wamwamuna wabadwa!’ Onani mutuwo |