Yobu 27:3 - Buku Lopatulika3 pakuti moyo wanga wonse ukali mwa ine, ndi mpweya wa Mulungu m'mphuno mwanga; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 pakuti moyo wanga wonse ukali mwa ine, ndi mpweya wa Mulungu m'mphuno mwanga; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Nthaŵi zonse pamene ndikupumabe, Mulungu namandipatsa mpweya wa moyo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 nthawi zonse pamene ndili ndi moyo, mpweya wa Mulungu uli mʼmphuno mwanga, Onani mutuwo |