Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 26:4 - Buku Lopatulika

4 Wafotokozera yani mau? Ndi mzimu wa yani unatuluka mwa iwe?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Wafotokozera yani mau? Ndi mzimu wa yani unatuluka mwa iwe?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Kodi ndani adzamva mau akoŵa? Nanga udazitenga kuti zonsezi?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Kodi wakuthandiza ndani kuti uyankhule mawu awa? Ndipo ndi mzimu wa yani umene unayankhula pakamwa pako?

Onani mutuwo Koperani




Yobu 26:4
9 Mawu Ofanana  

Ndamva kudzudzula kwakundichititsa manyazi, ndi mzimu wa nzeru yanga undiyankha.


Wampangira bwanji wopanda nzeruyu! Ndi kudziwitsa nzeru zenizeni mochuluka!


Adafawo anjenjemera pansi pamadzi ndi zokhalamo.


Pakuti ndadzazidwa ndi mau, ndi mzimu wa m'kati mwanga undifulumiza.


fumbi ndi kubwera pansi pomwe linali kale, mzimu ndi kubwera kwa Mulungu amene anaupereka.


Chifukwa chake ndikuuzani inu, kuti palibe munthu wakulankhula mwa Mzimu wa Mulungu, anena, Yesu ngwotembereredwa; ndipo palibe wina akhoza kunena, Yesu ali Ambuye, koma mwa Mzimu Woyera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa