Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 26:2 - Buku Lopatulika

2 Wamthandiza bwanji wopanda mphamvu. Kulipulumutsa dzanja losalimba!

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Wamthandiza bwanji wopanda mphamvu. Kulipulumutsa dzanja losalimba!

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 “Iwe, kodi wandithandiza ine munthu wosauka ndi wofookane ngati?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 “Wamuthandizadi munthu wopanda mphamvu! Walimbitsadi dzanja la munthu wofowoka!

Onani mutuwo Koperani




Yobu 26:2
15 Mawu Ofanana  

Ndipo pausana Eliya anawaseka, nati, Kwezani mau, popeza ndiye mulungu; kapena alikulingirira, kapena wapambuka, kapena ali paulendo, kaya agona, adzagalamuka.


Zoonadi inu ndinu anthu, ndi nzeru idzafa pamodzi ndi inu.


Koma Yobu anayankha, nati,


Wampangira bwanji wopanda nzeruyu! Ndi kudziwitsa nzeru zenizeni mochuluka!


Taonani, inu nonse munachiona; ndipo mugwidwa nazo zopanda pake chifukwa ninji?


Mphamvu yanga njotani kuti ndiyembekeze? Mathedwe anga ndi otani kuti ndipirire?


Kodi mphamvu yanga ndiyo mphamvu ya miyala? Mnofu wanga ndi mkuwa kodi?


Mulibe thandizo mwa ine ndekha; chipulumutso chandithawa.


Mau oongoka si ndiwo amphamvu? Koma kudzudzula kwanu mudzudzula chiyani?


Musanditaye mu ukalamba wanga; musandisiye, pakutha mphamvu yanga.


Iye anakhala upo ndi yani, ndipo ndani analangiza Iye ndi kumphunzitsa m'njira ya chiweruzo, ndi kumphunzitsa nzeru ndi kumuonetsa njira ya luntha?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa