Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 22:8 - Buku Lopatulika

8 Koma munthu mwini mphamvu, dziko ndi lake; ndi munthu wovomerezeka, anakhala momwemo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Koma munthu mwini mphamvu, dziko ndi lake; ndi munthu wovomerezeka, anakhala momwemo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Chifukwa cha mphamvu zako udalanda dziko lalikulu, chifukwa cha kudzikonda udakhazikika m'menemo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 ngakhale unali munthu wamphamvu, wokhala ndi malo akeake, munthu waulemu wake, wokhala mʼdzikomo.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 22:8
10 Mawu Ofanana  

Apita nao, ansembe atawafunkhira, nagubuduza amphamvu.


Kodi mukhalira kumodzi ndi Iye? Kodi mungamuimilire Mulungu pa mlandu?


popeza ndinaopa unyinji waukulu, ndi chipepulo cha mafuko chinandiopsetsa; potero ndinakhala chete osatuluka pakhomo panga.


Dziko lapansi laperekedwa m'dzanja la woipa; aphimba maso a oweruza ake. Ngati sindiye, pali yaninso?


Oipa amayenda mozungulirazungulira, potamanda iwo chonyansa mwa ana a anthu.


kapitao wa makumi asanu, ndi munthu wolemekezeka, ndi phungu, ndi mmisiri waluso, ndi wodziwa matsenga.


Nkhalamba ndi wolemekezeka ndiye mutu, ndi mneneri wophunzitsa zonama ndiye mchira.


Manja ao onse awiri agwira choipa kuchichita ndi changu; kalonga apempha, ndi woweruza aweruza chifukwa cha mphotho; ndi wamkuluyo angonena chosakaza moyo wake; ndipo achiluka pamodzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa