Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 22:5 - Buku Lopatulika

5 Zoipa zako sizichuluka kodi? Ndi mphulupulu zako sizikhala zosawerengeka kodi?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Zoipa zako sizichuluka kodi? Ndi mphulupulu zako sizikhala zosawerengeka kodi?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Kodi osati nchifukwa choti kuipa kwako nkwakukulu, ndipo kulakwa kwako nkopanda malire?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Kodi osati nʼchifukwa chakuti kuyipa kwako nʼkwakukulu? Kodi machimo ako si opanda malire?

Onani mutuwo Koperani




Yobu 22:5
12 Mawu Ofanana  

Mukakhala mphulupulu m'dzanja lako, uichotseretu kutali, ndi chisalungamo chisakhale m'mahema mwako.


nakufotokozere zinsinsi za nzeru, popeza zipindikapindika machitidwe ao! Chifukwa chake dziwa kuti Mulungu akuiwalira mphulupulu zina.


Taonani, ndidziwa maganizo anu, ndi chiwembu mundilingirira moipa.


Pamenepo amuna atatuwa analeka kumyankha Yobu; pakuti anali wolungama pamaso pake pa iye mwini.


Ndipo adapsa mtima Elihu mwana wa Barakele wa ku Buzi, wa chibale cha Ramu, adapsa mtima pa Yobu; pakuti anadziyesera yekha wolungama, wosati Mulungu.


Adapsa mtima pa mabwenzi ake atatu omwe, pakuti anasowa pomyankha; koma anamtsutsa Yobu kuti ali woipa.


Koma mukadzazidwa nazo zolingirira oipa, zolingirirazo ndi chiweruzo zidzakugwiranibe.


Adziwitsa zolowereza zake ndani? Mundimasule kwa zolakwa zobisika.


Pakuti zoipa zosawerengeka zandizinga, zochimwa zanga zandipeza kotero kuti sindikhoza kupenya; ziposa tsitsi la mutu wanga, ndipo wandichokera mtima.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa