Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 21:3 - Buku Lopatulika

3 Mundilole, ndinene nanenso; ndipo nditanena ine, sekani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Mundilole, ndinene nanenso; ndipo nditanena ine, sekani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Loleni ndilankhuleko, ndikatha kulankhula, munditonzeretonzere.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Ndiloleni ndiyankhule ndipo ndikatha kuyankhula munditonzetonze.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 21:3
10 Mawu Ofanana  

Kodi zotamanda zako ziwatseke anthu pakamwa? Useka kodi, wopanda munthu wakukuchititsapo manyazi?


Khalani chete, ndilekeni, kuti ndinene, chondifikira chifike.


Nchokoma kodi kuti Iye akusanthuleni? Kodi mudzamnyenga Iye monga munyenga munthu?


Iwo anandiyasamira pakamwa pao; anandiomba pama ndi kunditonza; asonkhana pamodzi kunditsutsa.


Mabwenzi anga andinyoza; koma diso langa lilirira misozi kwa Mulungu.


Zoonadi, ali nane ondiseka; ndi diso langa lili chipenyere m'kundiwindula kwao.


Mvetsetsani mau anga; ndi ichi chikhale chitonthozo chanu.


Taonani, inu nonse munachiona; ndipo mugwidwa nazo zopanda pake chifukwa ninji?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa