Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 21:2 - Buku Lopatulika

2 Mvetsetsani mau anga; ndi ichi chikhale chitonthozo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Mvetsetsani mau anga; ndi ichi chikhale chitonthozo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 “Mumvetsere bwino zimene ndikulankhula, kunditonthoza mtima kwanu kukhale komweko basi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 “Mvetserani bwino mawu anga; ichi chikhale chitonthozo changa chochokera kwa inu.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 21:2
14 Mawu Ofanana  

Mvetsetsani mau anga, ndi kunenetsa kwanga kumveke m'makutu mwanu.


Tamvani tsono kudzikanira kwanga, tamverani kudzinenera kwa milomo yanga.


Masangalatso a Mulungu akuchepera kodi? Kapena uli nacho chinsinsi kodi?


Ndamva zambiri zotere; inu nonse ndinu otonthoza mtima mondilemetsa.


Musaka mau kufikira liti? Zindikirani, ndi pamenepo tidzanena.


Pamenepo Yobu anayankha, nati,


Mundilole, ndinene nanenso; ndipo nditanena ine, sekani.


Komatu, Yobu, mumvere maneno anga, mutcherere khutu mau anga.


Tamverani mau anga, inu anzeru; munditcherere khutu inu akudziwa.


Bwanji inu mulikutayira ndalama chinthu chosadya, ndi kutayira malipiro anu zosakhutitsa? Mverani Ine mosamalitsa, nimudye chimene chili chabwino, moyo wanu nukondwere ndi zonona.


Mwa ichi tiyenera kusamaliradi zimene tidazimvazi kuti kapena tingatengedwe ndi kusiyana nazo.


Ndipo atamuuza Yotamu, anamuka iye naimirira pamutu paphiri la Gerizimu, nakweza mau ake, nafuula, nanena nao, Mundimvere ine, eni ake a ku Sekemu inu, kuti Mulungu amvere inu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa