Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 20:3 - Buku Lopatulika

3 Ndamva kudzudzula kwakundichititsa manyazi, ndi mzimu wa nzeru yanga undiyankha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndamva kudzudzula kwakundichititsa manyazi, ndi mzimu wa nzeru yanga undiyankha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Ndikumva mau ondidzudzula ndi ondinyoza, koma ndadziŵa kale m'mene ndingathe kuyankhira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Ndikumva kudzudzula kondinyoza, ndipo kumvetsetsa kwanga kwa zinthu kwandifulumiza kuti ndiyankhe.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 20:3
7 Mawu Ofanana  

muchite nalo mantha lupanga; pakuti mkwiyo utenga zolakwa za lupanga, kuti mudziwe pali chiweruzo.


Kakhumi aka mwandichititsa manyazi; mulibe manyazi kuti mundiumira mtima.


M'mwemo zolingirira zanga zindiyankha, chifukwa chake ndifulumidwa m'kati mwanga.


Ndidzakulangizani za dzanja la Mulungu; chokhala ndi Wamphamvuyonse sindidzachibisa.


Maneno anga awulula chiongoko cha mtima wanga, ndi monga umo idziwira milomo yanga idzanena zoona.


Pakamwa panga padzanena zanzeru; ndipo chilingiriro cha mtima wanga chidzakhala cha chidziwitso.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa