Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 18:3 - Buku Lopatulika

3 Tiyesedwa bwanji ngati nyama zakuthengo, ndi kukhala odetsedwa pamaso panu?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Tiyesedwa bwanji ngati nyama za kuthengo, ndi kukhala odetsedwa pamaso panu?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Chifukwa chiyani ukutiyesa opusa ngati ng'ombe? Chifukwa chiyani tikuwoneka ngati opanda nzeru m'maso mwako?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Chifukwa chiyani ukutiyesa ngati ngʼombe ndi kuoneka ngati opusa mʼmaso mwako?

Onani mutuwo Koperani




Yobu 18:3
9 Mawu Ofanana  

Koma bwerani inu nonse, idzani tsono; pakuti sindipeza mwa inu wanzeru.


Pakuti mwabisira mtima wao nzeru; chifukwa chake simudzawakuza.


Musaka mau kufikira liti? Zindikirani, ndi pamenepo tidzanena.


Iwe wodzing'amba mumkwiyo mwako, kodi dziko lapansi lisiyidwe chifukwa cha iwe? Kapena thanthwe lisunthike m'malo mwake?


ndinali wam'thengo, wosadziwa kanthu; ndinali ngati nyama pamaso panu.


Ndinati mumtima mwanga, kuti izi zichitika ndi ana a anthu, kuti Mulungu awayese ndi kuti akazindikire eni ake kuti ndiwo nyama zakuthengo.


M'chikondano cha anzanu wina ndi mnzake mukondane ndi chikondi chenicheni; mutsogolerane ndi kuchitira wina mnzake ulemu;


Amkwapule kufikira makumi anai, asaonjezepo; pakuti, akaonjezapo ndi kumkwapula mikwapulo yambiri, angapeputse mbale wanu pamaso panu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa